Yohane 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anamuyankha kuti: “Yesu Mnazareti.”+ Iye anati: “Ndine amene.” Yudasi womupereka uja,+ analinso nawo pamenepo. Machitidwe 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anati: “Mbuyanga, ndinu ndani kodi?” Anamuyankha kuti: “Ndine Yesu, amene iwe ukumuzunza.+ Machitidwe 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ine ndinati, ‘Mbuyanga, ndinu ndani kodi?’ Ndipo Ambuye anati, ‘Ndine Yesu, amene iwe ukumuzunza.+
5 Iwo anamuyankha kuti: “Yesu Mnazareti.”+ Iye anati: “Ndine amene.” Yudasi womupereka uja,+ analinso nawo pamenepo.
15 Koma ine ndinati, ‘Mbuyanga, ndinu ndani kodi?’ Ndipo Ambuye anati, ‘Ndine Yesu, amene iwe ukumuzunza.+