Machitidwe 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anati: “Mbuyanga, ndinu ndani kodi?” Anamuyankha kuti: “Ndine Yesu, amene iwe ukumuzunza.+ Machitidwe 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndinayankha kuti, ‘Ndinu ndani, Mbuyanga?’ Ndipo anandiuza kuti, ‘Ndine Yesu Mnazareti, amene iwe ukumuzunza.’+
8 Ine ndinayankha kuti, ‘Ndinu ndani, Mbuyanga?’ Ndipo anandiuza kuti, ‘Ndine Yesu Mnazareti, amene iwe ukumuzunza.’+