Machitidwe 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Saulo anaimirira, koma ngakhale anali atatsegula maso, sanali kuona chilichonse.+ Choncho anamugwira dzanja ndi kumulondolera njira ndipo analowa naye mu Damasiko.
8 Tsopano Saulo anaimirira, koma ngakhale anali atatsegula maso, sanali kuona chilichonse.+ Choncho anamugwira dzanja ndi kumulondolera njira ndipo analowa naye mu Damasiko.