Machitidwe 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma popeza sindinali kuona chilichonse chifukwa cha ulemerero wa kuwalako, amuna amene ndinali nawo limodzi aja, anandigwira dzanja mpaka kukafika ku Damasiko.+
11 Koma popeza sindinali kuona chilichonse chifukwa cha ulemerero wa kuwalako, amuna amene ndinali nawo limodzi aja, anandigwira dzanja mpaka kukafika ku Damasiko.+