Machitidwe 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma Paulo anawauza kuti: “Iwo atikwapula pamaso pa anthu ndi kutiponya m’ndende popanda kuzenga mlandu wathu, chikhalirecho ndife Aroma.+ Kodi tsopano akutitulutsa mseri? Ayi, zimenezo sizitheka! Abwere eniakewo adzatitulutse okha.”
37 Koma Paulo anawauza kuti: “Iwo atikwapula pamaso pa anthu ndi kutiponya m’ndende popanda kuzenga mlandu wathu, chikhalirecho ndife Aroma.+ Kodi tsopano akutitulutsa mseri? Ayi, zimenezo sizitheka! Abwere eniakewo adzatitulutse okha.”