Machitidwe 22:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma atamugoneka kuti amukwapule, Paulo anafunsa kapitawo wa asilikali amene anali ataima pamenepo kuti: “Kodi anthu inu, malamulo amakulolani kukwapula munthu amene ndi Mroma,+ mlandu wake usanazengedwe?” Machitidwe 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu uyu anagwidwa ndi Ayuda ndipo anali pafupi kumupha. Koma ine ndinafika mwadzidzidzi ndi gulu la asilikali n’kumulanditsa,+ chifukwa ndinamva kuti iyeyu ndi Mroma.+
25 Koma atamugoneka kuti amukwapule, Paulo anafunsa kapitawo wa asilikali amene anali ataima pamenepo kuti: “Kodi anthu inu, malamulo amakulolani kukwapula munthu amene ndi Mroma,+ mlandu wake usanazengedwe?”
27 Munthu uyu anagwidwa ndi Ayuda ndipo anali pafupi kumupha. Koma ine ndinafika mwadzidzidzi ndi gulu la asilikali n’kumulanditsa,+ chifukwa ndinamva kuti iyeyu ndi Mroma.+