Yesaya 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+ Machitidwe 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithudi, panalibe ngakhale mmodzi wosowa kanthu pakati pawo.+ Onse amene anali ndi minda kapena nyumba, anali kuzigulitsa ndi kubweretsa ndalamazo,
7 Ndimafunanso kuti muzigawira chakudya chanu anthu anjala,+ ndiponso kuti muziitanira m’nyumba zanu anthu osautsika ndi osowa pokhala.+ Ndimafuna kuti mukaona munthu wosavala muzimuveka+ ndiponso kuti musamadzibise kwa abale anu.+
34 Ndithudi, panalibe ngakhale mmodzi wosowa kanthu pakati pawo.+ Onse amene anali ndi minda kapena nyumba, anali kuzigulitsa ndi kubweretsa ndalamazo,