Deuteronomo 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati panu pasapezeke munthu wosauka, chifukwa Yehova adzakudalitsa ndithu+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti likhale cholowa chako.+ Machitidwe 2:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Anali kugulitsa malo awo ndi zina zimene anali nazo,+ n’kugawa kwa onse zimene apeza, aliyense malinga ndi kusowa kwake.+ 1 Yohane 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo,+ n’kuona m’bale wake zikumusowa,+ koma osamusonyeza m’bale wakeyo chifundo chachikulu,+ kodi munthu ameneyu amakonda Mulungu?+
4 Pakati panu pasapezeke munthu wosauka, chifukwa Yehova adzakudalitsa ndithu+ m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa kuti likhale cholowa chako.+
45 Anali kugulitsa malo awo ndi zina zimene anali nazo,+ n’kugawa kwa onse zimene apeza, aliyense malinga ndi kusowa kwake.+
17 Koma aliyense amene ali ndi zinthu zofunika pa moyo,+ n’kuona m’bale wake zikumusowa,+ koma osamusonyeza m’bale wakeyo chifundo chachikulu,+ kodi munthu ameneyu amakonda Mulungu?+