Deuteronomo 25:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+ Yohane 7:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 “Chilamulo chathu sichiweruza munthu asanafotokoze maganizo ake choyamba+ ndi kudziwa zochita zake, chimatero ngati?”
25 “Amuna akakangana+ n’kupita kwa oweruza,+ oweruzawo azigamula mlanduwo. Wolungama azimuweruza kuti ndi wolungama ndipo woipa azimuweruza kuti ndi woipa.+
51 “Chilamulo chathu sichiweruza munthu asanafotokoze maganizo ake choyamba+ ndi kudziwa zochita zake, chimatero ngati?”