Machitidwe 21:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Pamenepo mkulu wa asilikali uja anafika pafupi ndi kumugwira ndipo analamula kuti amumange ndi maunyolo awiri.+ Ndiyeno anafunsa za iye kuti anali ndani ndiponso zimene anachita.
33 Pamenepo mkulu wa asilikali uja anafika pafupi ndi kumugwira ndipo analamula kuti amumange ndi maunyolo awiri.+ Ndiyeno anafunsa za iye kuti anali ndani ndiponso zimene anachita.