Machitidwe 23:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndiyeno anaitanitsa akapitawo awiri a asilikali ndi kuwauza kuti: “Uzani asilikali 200 kuti akonzekere kuyenda mpaka kukalowa mu Kaisareya cha m’ma 9 koloko* usiku uno. Pakhalenso amuna 70 okwera mahatchi* ndi asilikali 200 a mikondo.
23 Ndiyeno anaitanitsa akapitawo awiri a asilikali ndi kuwauza kuti: “Uzani asilikali 200 kuti akonzekere kuyenda mpaka kukalowa mu Kaisareya cha m’ma 9 koloko* usiku uno. Pakhalenso amuna 70 okwera mahatchi* ndi asilikali 200 a mikondo.