Mateyu 5:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine. Machitidwe 16:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atafika nawo kwa akuluakulu a boma, ananena kuti: “Anthu awa akusokoneza kwambiri+ mzinda wathu, chikhalirecho iwowa ndi Ayuda. Machitidwe 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Atalephera kuwapeza, anakokera Yasoni ndi abale ena kwa olamulira a mzindawo, akufuula kuti: “Anthu awa amene abweretsa mavuto+ padziko lapansi kumene kuli anthu, tsopano akupezekanso kuno,
11 “Ndinu odala pamene anthu akukunyozani+ ndi kukuzunzani,+ komanso kukunamizirani zoipa zilizonse chifukwa cha ine.
20 Atafika nawo kwa akuluakulu a boma, ananena kuti: “Anthu awa akusokoneza kwambiri+ mzinda wathu, chikhalirecho iwowa ndi Ayuda.
6 Atalephera kuwapeza, anakokera Yasoni ndi abale ena kwa olamulira a mzindawo, akufuula kuti: “Anthu awa amene abweretsa mavuto+ padziko lapansi kumene kuli anthu, tsopano akupezekanso kuno,