Mateyu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inde, adzakutengerani kwa abwanamkubwa ndi mafumu+ chifukwa cha ine, kuti ukhale umboni+ kwa iwo ndi kwa anthu a mitundu ina. 1 Petulo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma vomerezani m’mitima mwanu kuti Khristu ndi Ambuye ndiponso kuti ndi woyera.+ Khalani okonzeka nthawi zonse kuyankha+ aliyense amene wakufunsani za chiyembekezo chimene muli nacho, koma ayankheni ndi mtima wofatsa+ ndiponso mwaulemu kwambiri.
18 Inde, adzakutengerani kwa abwanamkubwa ndi mafumu+ chifukwa cha ine, kuti ukhale umboni+ kwa iwo ndi kwa anthu a mitundu ina.
15 Koma vomerezani m’mitima mwanu kuti Khristu ndi Ambuye ndiponso kuti ndi woyera.+ Khalani okonzeka nthawi zonse kuyankha+ aliyense amene wakufunsani za chiyembekezo chimene muli nacho, koma ayankheni ndi mtima wofatsa+ ndiponso mwaulemu kwambiri.