Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Machitidwe 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pamenepo Petulo, atadzazidwa ndi mzimu woyera,+ anawayankha kuti:

      “Olamulira anthu ndiponso akulu inu,

  • Machitidwe 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamene bwanamkubwayo anagwedezera Paulo mutu kuti alankhule, Paulo anayankha kuti:

      “Ine podziwa bwino kuti mwakhala woweruza wa mtundu uwu kwa zaka zambiri, ndine wokondwa kuti ndilankhule podziteteza+ pa zimene akundinenezazi.

  • Machitidwe 25:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 M’mawa wake, Agiripa ndi Berenike anabwera ndi ulemu waukulu wachifumu.+ Analowa m’chipinda chosonkhanira pamodzi ndi akuluakulu a asilikali komanso akuluakulu a mumzindawo, ndipo Fesito atalamula, anamubweretsa Paulo.

  • Machitidwe 26:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma Paulo anati: “Wolemekezeka a Fesito, inetu sindinachite misala ayi, koma ndikulankhula mawu a choonadi ndiponso anzeru.

  • Machitidwe 27:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 ndi kunena kuti, ‘Usaope Paulo. Uyenera kukaima pamaso pa Kaisara,+ ndipo taona! Chifukwa cha iwe, Mulungu mokoma mtima adzapulumutsa onse amene uli nawo pa ulendowu.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena