Machitidwe 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anati: “Amene ali ndi maudindo pakati panu, tipitire limodzi kuti ngati pali cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu akamuimbe mlandu.”+
5 Ndiyeno anati: “Amene ali ndi maudindo pakati panu, tipitire limodzi kuti ngati pali cholakwa chilichonse mwa munthu ameneyu akamuimbe mlandu.”+