Machitidwe 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma pofuna kuti Ayudawo amukonde,+ Fesito anayankha Paulo kuti: “Kodi ukufuna kupita ku Yerusalemu, kuti nkhani imeneyi ikaweruzidwe kumeneko pamaso panga?”+
9 Koma pofuna kuti Ayudawo amukonde,+ Fesito anayankha Paulo kuti: “Kodi ukufuna kupita ku Yerusalemu, kuti nkhani imeneyi ikaweruzidwe kumeneko pamaso panga?”+