Machitidwe 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma ndilibe chenicheni chimene ndingalembere Mbuyanga chokhudza munthuyu. Choncho ndamubweretsa pamaso panu, makamaka pamaso pa inu, Mfumu Agiripa, kuti mukamufunsa za nkhaniyi,+ ndipeze cholemba.
26 Koma ndilibe chenicheni chimene ndingalembere Mbuyanga chokhudza munthuyu. Choncho ndamubweretsa pamaso panu, makamaka pamaso pa inu, Mfumu Agiripa, kuti mukamufunsa za nkhaniyi,+ ndipeze cholemba.