Machitidwe 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo atakhala nthawi yaitali osadya kanthu, Paulo anaimirira pakati pawo+ ndi kunena kuti: “Anthu inu, mukanamvera malangizo anga, osachoka ku Kerete kuja, ndithu zinthu sizikanawonongeka ndi kutayika chonchi.+
21 Ndipo atakhala nthawi yaitali osadya kanthu, Paulo anaimirira pakati pawo+ ndi kunena kuti: “Anthu inu, mukanamvera malangizo anga, osachoka ku Kerete kuja, ndithu zinthu sizikanawonongeka ndi kutayika chonchi.+