-
Machitidwe 27:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Komabe, ndikukuuzani kuti mukhale osangalala, chifukwa palibe aliyense wa inu amene ataye moyo wake, koma ngalawa yokhayi iwonongeka.
-