Machitidwe 27:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano tinayenda m’mphepete mwa chilumba china chaching’ono chotchedwa Kauda chimene chinali kutitchinjiriza ku mphepo. Komabe tinali kulephera kuwongolera bwato laling’ono limene ngalawayo inali kukoka.+
16 Tsopano tinayenda m’mphepete mwa chilumba china chaching’ono chotchedwa Kauda chimene chinali kutitchinjiriza ku mphepo. Komabe tinali kulephera kuwongolera bwato laling’ono limene ngalawayo inali kukoka.+