Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 15:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 anatenga mitanda 7 ya mkate ija ndi nsomba zija. Atayamika, anainyemanyema n’kupatsa ophunzirawo ndipo iwo anagawira khamu la anthulo.+

  • Maliko 8:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno anauza anthuwo kuti akhale pansi. Kenako, anatenga mitanda 7 ya mkate ija, ndi kuyamika.+ Atatero anainyemanyema n’kupatsa ophunzira ake kuti agawe, ndipo iwo anagawira khamu la anthulo.+

  • Yohane 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Yesu anatenga mitanda ya mkate ija. Atayamika, anaigawira kwa anthu onse amene anakhala pansi aja. Chimodzimodzinso ndi tinsomba tija, anatigawira kwa anthuwo mmene aliyense anafunira.+

  • Aroma 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Amene amasunga tsiku amalisungira kulemekeza Yehova. Amene amadya, amadya kuti alemekeze Yehova,+ chifukwa amayamika Mulungu.+ Amene sadya, sadya pofuna kulemekeza Yehova,+ chifukwa nayenso amayamika Mulungu.+

  • 1 Timoteyo 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndikutero chifukwa chakuti chilichonse cholengedwa ndi Mulungu n’chabwino,+ ndipo palibe chimene chiyenera kukanidwa+ ngati chalandiridwa moyamikira,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena