Maliko 7:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wogontha komanso wovutika kulankhula. Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.+ Machitidwe 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mulungu anapitiriza kuchita ntchito zamphamvu zodabwitsa kudzera mwa Paulo.+ 1 Akorinto 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwa mzimu womwewonso wina amapatsidwa chikhulupiriro,+ wina mphatso za kuchiritsa.+
32 Kumeneko anthu anam’bweretsera munthu wogontha komanso wovutika kulankhula. Iwo anamupempha kuti aike dzanja lake pa munthuyo.+