Machitidwe 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumeneko kapitawo wa asilikali anapeza ngalawa yochokera ku Alekizandiriya+ imene inali kupita ku Italiya, ndipo anatikweza mmenemo.
6 Kumeneko kapitawo wa asilikali anapeza ngalawa yochokera ku Alekizandiriya+ imene inali kupita ku Italiya, ndipo anatikweza mmenemo.