Machitidwe 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Patapita miyezi itatu, tinanyamuka pangalawa ya ku Alekizandiriya.+ Ngalawa imeneyi inaima pachilumbapo kuyembekezera kuti nyengo yachisanu ithe, ndipo inali ndi chizindikiro cha “Ana Amapasa a Zeu.”
11 Patapita miyezi itatu, tinanyamuka pangalawa ya ku Alekizandiriya.+ Ngalawa imeneyi inaima pachilumbapo kuyembekezera kuti nyengo yachisanu ithe, ndipo inali ndi chizindikiro cha “Ana Amapasa a Zeu.”