Machitidwe 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kunena zoona, inu mfumu amene ndikulankhula nanu mwaufulu chotere, mukudziwa bwino zimenezi. Ndili wotsimikiza kuti palibe ngakhale chimodzi mwa zinthu zimenezi, chimene simunachizindikire, pakuti izi sizinachitikire mseri.+ Aefeso 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 kuphatikizapo ineyo. Chitani zimenezi kuti ndikatsegula pakamwa panga kuti ndilankhule, ndizitha kulankhula+ mwaufulu+ kuti ndidziwitse ena chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+
26 Kunena zoona, inu mfumu amene ndikulankhula nanu mwaufulu chotere, mukudziwa bwino zimenezi. Ndili wotsimikiza kuti palibe ngakhale chimodzi mwa zinthu zimenezi, chimene simunachizindikire, pakuti izi sizinachitikire mseri.+
19 kuphatikizapo ineyo. Chitani zimenezi kuti ndikatsegula pakamwa panga kuti ndilankhule, ndizitha kulankhula+ mwaufulu+ kuti ndidziwitse ena chinsinsi chopatulika cha uthenga wabwino,+