Mateyu 27:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ ndi kuti Yesu aphedwe. Luka 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma khamu lonse linafuulira pamodzi kuti: “Ameneyu muthane naye basi,+ koma ife mutimasulire Baraba!”+
20 Koma ansembe aakulu limodzi ndi akulu analimbikitsa anthu kupempha kuti awamasulire Baraba,+ ndi kuti Yesu aphedwe.
18 Koma khamu lonse linafuulira pamodzi kuti: “Ameneyu muthane naye basi,+ koma ife mutimasulire Baraba!”+