Luka 23:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 [[Koma Yesu anati: “Atate, akhululukireni,+ chifukwa sakudziwa chimene akuchita.”]]* Ndipo iwo anagawana malaya ake mwa kuchita maere.+ Yohane 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma adzachita zimenezi chifukwa sanadziwe Atate kapena ine.+ 1 Timoteyo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anatero ngakhale kuti kale ndinali wonyoza Mulungu, wozunza anthu ake+ ndiponso wachipongwe.+ Komabe anandichitira chifundo+ chifukwa ndinali wosadziwa+ ndi wopanda chikhulupiriro.
34 [[Koma Yesu anati: “Atate, akhululukireni,+ chifukwa sakudziwa chimene akuchita.”]]* Ndipo iwo anagawana malaya ake mwa kuchita maere.+
13 Anatero ngakhale kuti kale ndinali wonyoza Mulungu, wozunza anthu ake+ ndiponso wachipongwe.+ Komabe anandichitira chifundo+ chifukwa ndinali wosadziwa+ ndi wopanda chikhulupiriro.