Deuteronomo 18:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamula.+ Machitidwe 7:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 “Ameneyu ndi Mose amene anauza ana a Isiraeli kuti, ‘Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati pa abale anu.’+
18 Ndidzawapatsa mneneri ngati iwe kuchokera pakati pa abale awo.+ Ndidzaika mawu anga m’kamwa mwake,+ ndipo adzawauza zonse zimene ndidzamulamula.+
37 “Ameneyu ndi Mose amene anauza ana a Isiraeli kuti, ‘Mulungu adzakupatsani mneneri ngati ine, kuchokera pakati pa abale anu.’+