Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Choncho Mose anakhalabe m’phirimo ndi Yehova masiku 40, usana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Mawu Khumi,* pamiyala yosemayo.+

  • Numeri 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Moseyo anali munthu wofatsa kwambiri+ kuposa anthu onse amene anali padziko lapansi.

  • Malaki 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Taonani! Ine nditumiza mthenga wanga+ ndipo iye adzandikonzera njira.+ Mwadzidzidzi, Ambuye woona, amene anthu inu mukumufunafuna, adzabwera kukachisi+ Wake.+ Adzabwera ndi mthenga+ wa pangano+ amene mukumuyembekezera mosangalala.+ Iye adzabwera ndithu,” watero Yehova wa makamu.+

  • Mateyu 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Atasala kudya masiku 40 usana ndi usiku,+ anamva njala.

  • Mateyu 11:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Senzani goli+ langa ndipo phunzirani kwa ine,+ chifukwa ndine wofatsa+ ndi wodzichepetsa, ndipo mudzatsitsimulidwa,+

  • Luka 24:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pamenepo anayamba kuwatanthauzira zinthu zokhudza iyeyo m’Malemba onse, kuyambira ndi Zolemba za Mose+ ndi za aneneri zonse.+

  • Luka 24:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 Ndiyeno anawauza kuti: “Pamene ndinali nanu limodzi+ ndinakuuzani mawu akuti, zonse zokhudza ine zolembedwa m’chilamulo cha Mose, m’Zolemba za aneneri+ ndi m’Masalimo+ ziyenera kukwaniritsidwa.”

  • Yohane 5:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Ndipo ngati mukanakhulupirira Mose, mukanakhulupiriranso ine, pakuti iyeyo analemba za ine.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena