Luka 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+ Yohane 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+
2 M’masiku amenewo Anasi anali wansembe wamkulu ndipo Kayafa+ anali mkulu wa ansembe. Pa nthawiyo mawu a Mulungu anafika kwa Yohane+ mwana wa Zekariya m’chipululu.+
13 Choyamba anapita naye kwa Anasi, pakuti anali mpongozi wa Kayafa, amene anali mkulu wa ansembe chaka chimenecho.+