Machitidwe 2:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Onse amene anakhala okhulupirira anasonkhana pamodzi ndipo zinthu zonse zimene anali nazo zinali za onse.+
44 Onse amene anakhala okhulupirira anasonkhana pamodzi ndipo zinthu zonse zimene anali nazo zinali za onse.+