Machitidwe 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo onse amene anakhulupirira anakhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+ Panalibe ngakhale mmodzi wonena kuti zinthu zimene anali nazo zinali zayekha. Zonse zimene anali nazo zinali za onse.+
32 Ndipo onse amene anakhulupirira anakhala ndi mtima umodzi ndi maganizo amodzi.+ Panalibe ngakhale mmodzi wonena kuti zinthu zimene anali nazo zinali zayekha. Zonse zimene anali nazo zinali za onse.+