Mateyu 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye sali pano chifukwa wauka kwa akufa+ monga ananenera. Bwerani muone pamene anagona. Maliko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho. Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anapachikidwa.+ Iyetu wauka kwa akufa,+ salinso muno ayi. Taonani! Si apa pamene anamugoneka!+ Machitidwe 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatsiriza kunena zimenezi, Mulungu anamunyamula kupita m’mlengalenga iwo akuonerera,+ ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+
6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho. Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anapachikidwa.+ Iyetu wauka kwa akufa,+ salinso muno ayi. Taonani! Si apa pamene anamugoneka!+
9 Atatsiriza kunena zimenezi, Mulungu anamunyamula kupita m’mlengalenga iwo akuonerera,+ ndipo mtambo unamuphimba moti sanathenso kumuona.+