Machitidwe 10:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Atatero anawalamula kuti abatizidwe m’dzina la Yesu Khristu.+ Pamenepo iwo anamupempha kuti akhalebe nawo masiku angapo. Machitidwe 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo anawafunsa kuti: “Kodi munalandira mzimu woyera+ mutakhala okhulupirira?” Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu sitinamvepo kuti kuli mzimu woyera.”+
48 Atatero anawalamula kuti abatizidwe m’dzina la Yesu Khristu.+ Pamenepo iwo anamupempha kuti akhalebe nawo masiku angapo.
2 ndipo anawafunsa kuti: “Kodi munalandira mzimu woyera+ mutakhala okhulupirira?” Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu sitinamvepo kuti kuli mzimu woyera.”+