Machitidwe 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno anawaimiritsa pamaso pa atumwiwo, ndipo atapemphera, atumwiwo anaika manja+ awo pa iwo. Machitidwe 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Paulo atawaika manja,+ mzimu woyera unafika pa iwo, ndipo anayamba kulankhula malilime ndi kunenera.+ 2 Timoteyo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pa chifukwa chimenechi, ndikukukumbutsa kuti mphatso+ ya Mulungu imene ili mwa iwe, yomwe unailandira pamene ndinaika manja anga pa iwe,+ uikolezere ngati moto.+
6 Ndiyeno Paulo atawaika manja,+ mzimu woyera unafika pa iwo, ndipo anayamba kulankhula malilime ndi kunenera.+
6 Pa chifukwa chimenechi, ndikukukumbutsa kuti mphatso+ ya Mulungu imene ili mwa iwe, yomwe unailandira pamene ndinaika manja anga pa iwe,+ uikolezere ngati moto.+