Mika 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+ 1 Timoteyo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zimayambitsanso mapokoso achiwawa pa zinthu zazing’ono pakati pa anthu opotoka maganizo+ ndi osadziwa choonadi,+ poganiza kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi njira yopezera phindu.+
11 Atsogoleri a mumzindawo saweruza asanalandire chiphuphu+ ndipo ansembe ake amaphunzitsa kuti apeze malipiro.+ Aneneri ake amalosera kuti apeze ndalama.+ Komatu iwo amadalira Yehova ndipo amanena kuti: “Kodi Yehova sali pakati pathu?+ Choncho tsoka silidzatigwera.”+
5 Zimayambitsanso mapokoso achiwawa pa zinthu zazing’ono pakati pa anthu opotoka maganizo+ ndi osadziwa choonadi,+ poganiza kuti kukhala wodzipereka kwa Mulungu ndi njira yopezera phindu.+