Machitidwe 22:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma ndili m’njira, ndikuyandikira ku Damasiko, dzuwa lili pamutu, mwadzidzidzi kuwala kwakukulu kochokera kumwamba kunangoti ngwee! kuzungulira pamene ine ndinali.+
6 “Koma ndili m’njira, ndikuyandikira ku Damasiko, dzuwa lili pamutu, mwadzidzidzi kuwala kwakukulu kochokera kumwamba kunangoti ngwee! kuzungulira pamene ine ndinali.+