Machitidwe 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.” Aroma 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Ndine Paulo kapolo+ wa Yesu Khristu, woitanidwa+ kuti ndikhale mtumwi,+ ndiponso wosankhidwa kuti ndilalikire uthenga wabwino wa Mulungu.+ 1 Timoteyo 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikuyamika Khristu Yesu Ambuye wathu amene anandipatsa mphamvu poona kuti ndine wokhulupirika,+ ndipo anandipatsa utumiki.+
2 Pamene anali kutumikira+ Yehova ndi kusala kudya, mzimu woyera unati: “Mwa anthu onse, mundipatulire Baranaba ndi Saulo+ kuti agwire ntchito imene ndinawaitanira.”
1 Ndine Paulo kapolo+ wa Yesu Khristu, woitanidwa+ kuti ndikhale mtumwi,+ ndiponso wosankhidwa kuti ndilalikire uthenga wabwino wa Mulungu.+
12 Ndikuyamika Khristu Yesu Ambuye wathu amene anandipatsa mphamvu poona kuti ndine wokhulupirika,+ ndipo anandipatsa utumiki.+