Machitidwe 4:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Choncho Yosefe, amene atumwiwo anamutchanso Baranaba,+ dzina limene polimasulira limatanthauza, Mwana wa Chitonthozo, amene anali Mlevi, komanso mbadwa ya ku Kupuro,
36 Choncho Yosefe, amene atumwiwo anamutchanso Baranaba,+ dzina limene polimasulira limatanthauza, Mwana wa Chitonthozo, amene anali Mlevi, komanso mbadwa ya ku Kupuro,