Machitidwe 9:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yomweyo anayamba kulalikira za Yesu m’masunagoge,+ kuti Ameneyu ndiye Mwana wa Mulungu.