Mateyu 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Maonekedwe ake anali ngati a mphezi,+ ndipo zovala zake zinali zoyera mbee!+ Machitidwe 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mmene iwo anali kuyang’anitsitsa kuthambo pamene iye anali kukwera kumwamba,+ panaonekera amuna awiri ovala zoyera+ ataimirira pambali pawo.
10 Mmene iwo anali kuyang’anitsitsa kuthambo pamene iye anali kukwera kumwamba,+ panaonekera amuna awiri ovala zoyera+ ataimirira pambali pawo.