Machitidwe 10:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+ Agalatiya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti asanafike anthu ena ochokera kwa Yakobo,+ iye anali kudya+ limodzi ndi anthu a mitundu ina, koma anthuwo atafika, iye anadzipatula ndipo anasiya kuchitira nawo zinthu limodzi, chifukwa ankaopa+ anthu odulidwawo.+
45 Ndipo okhulupirika amene anabwera ndi Petulo, amene anali odulidwa anadabwa, chifukwa mphatso yaulere ya mzimu woyera inalinso kuthiridwa pa anthu a mitundu ina.+
12 Pakuti asanafike anthu ena ochokera kwa Yakobo,+ iye anali kudya+ limodzi ndi anthu a mitundu ina, koma anthuwo atafika, iye anadzipatula ndipo anasiya kuchitira nawo zinthu limodzi, chifukwa ankaopa+ anthu odulidwawo.+