Machitidwe 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamenepo Koneliyo anati: “Masiku anayi apitawo kuchokera pa ola lino, ndinali kupemphera m’nyumba mwanga cha m’ma 3 koloko masana.+ Mwadzidzidzi munthu wovala zowala+ anaimirira pamaso panga.
30 Pamenepo Koneliyo anati: “Masiku anayi apitawo kuchokera pa ola lino, ndinali kupemphera m’nyumba mwanga cha m’ma 3 koloko masana.+ Mwadzidzidzi munthu wovala zowala+ anaimirira pamaso panga.