Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 44:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti ndidzapatsa madzi munthu waludzu,+ ndipo ndidzaika timitsinje tamadzi pamalo ouma.+ Ndidzatsanulira mzimu wanga pambewu yako+ ndi madalitso anga pa mbadwa zako.

  • Yoweli 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Zimenezi zikadzachitika ndidzatsanulira mzimu wanga+ pa chamoyo chilichonse,+ ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi+ adzanenera. Amuna achikulire adzalota maloto ndipo anyamata adzaona masomphenya.

  • Yohane 1:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Inenso sindinali kumudziwa, koma Amene anandituma+ kudzabatiza m’madzi anandiuza kuti, ‘Ukadzaona mzimu ukutsika ndi kukhazikika pa munthu wina, ameneyo ndiye wobatiza ndi mzimu woyera.’+

  • Machitidwe 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 ‘“Ndipo m’masiku otsiriza,” akutero Mulungu, “ndidzatsanulira mbali ya mzimu wanga+ pa anthu osiyanasiyana, ndipo ana anu aamuna ndi ana anu aakazi adzanenera. Anyamata anu adzaona masomphenya, ndipo amuna achikulire adzalota maloto.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena