Machitidwe 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chilumba cha Kupuro+ chitayamba kuonekera, tinachisiya kumanzere ndi kupitiriza ulendo wathu kulowera ku Siriya.+ Tinaima ku Turo, chifukwa kumeneko ngalawa inafunika kutsitsa katundu.+
3 Chilumba cha Kupuro+ chitayamba kuonekera, tinachisiya kumanzere ndi kupitiriza ulendo wathu kulowera ku Siriya.+ Tinaima ku Turo, chifukwa kumeneko ngalawa inafunika kutsitsa katundu.+