Yohane 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kumbukirani mawu amene ndinakuuzani aja, kapolo sali wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso anu. Machitidwe 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho anawagwira ndi kuwasunga m’ndende mpaka tsiku lotsatira,+ chifukwa anali kale madzulo.
20 Kumbukirani mawu amene ndinakuuzani aja, kapolo sali wamkulu kuposa mbuye wake. Ngati anazunza ine, inunso adzakuzunzani.+ Ngati asunga mawu anga, adzasunganso anu.