Machitidwe 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma Ayuda ochokera ku Tesalonika atamva kuti Paulo akufalitsanso mawu a Mulungu ku Bereya, anapitanso kumeneko kukayambitsa chipolowe+ ndi kuchititsa anthuwo kukwiyira+ atumwiwo.
13 Koma Ayuda ochokera ku Tesalonika atamva kuti Paulo akufalitsanso mawu a Mulungu ku Bereya, anapitanso kumeneko kukayambitsa chipolowe+ ndi kuchititsa anthuwo kukwiyira+ atumwiwo.