Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti simudzasiya moyo wanga m’Manda.+

      Simudzalola kuti wokhulupirika wanu aone dzenje.+

  • Machitidwe 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Chotero munapha Mtumiki Wamkulu wa moyo,+ koma Mulungu anamuukitsa kwa akufa, ndipo ife ndife mboni za choonadi chimenechi.+

  • Aroma 4:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 komanso ife amene tidzayesedwa otero, chifukwa chakuti timakhulupirira iye amene anaukitsa Yesu Ambuye wathu kwa akufa.+

  • 1 Akorinto 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma Mulungu anaukitsa Ambuye+ kwa akufa+ ndipo adzaukitsanso ife mwa mphamvu yake.+

  • Akolose 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zinatero popeza munakwiriridwa naye limodzi mwa kubatizidwa ubatizo wofanana ndi wake,+ ndipo chifukwa choti muli naye pa ubwenzi, munaukitsidwa+ naye limodzi kudzera m’chikhulupiriro chimene muli nacho+ mu zinthu zimene zinachitika chifukwa cha mphamvu+ ya Mulungu, amene anamuukitsa kwa akufa.+

  • Aheberi 13:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Tsopano, Mulungu wamtendere,+ amene anaukitsa kwa akufa+ m’busa wamkulu+ wa nkhosa+ wokhala ndi magazi a pangano losatha,+ Ambuye wathu Yesu,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena