2 Akorinto 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kuti ndikadzacheza nanu pang’ono ndidzapite ku Makedoniya,+ ndipo ndikadzachoka ku Makedoniya ndidzabwerenso kwa inu+ kuti mudzandiperekeze+ popita ku Yudeya. 2 Akorinto 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 mtima wanga sunakhazikike chifukwa Tito+ m’bale wanga sindinamupeze. Ndiye ndinatsanzikana ndi abale kumeneko, n’kupita ku Makedoniya.+
16 Kuti ndikadzacheza nanu pang’ono ndidzapite ku Makedoniya,+ ndipo ndikadzachoka ku Makedoniya ndidzabwerenso kwa inu+ kuti mudzandiperekeze+ popita ku Yudeya.
13 mtima wanga sunakhazikike chifukwa Tito+ m’bale wanga sindinamupeze. Ndiye ndinatsanzikana ndi abale kumeneko, n’kupita ku Makedoniya.+