Machitidwe 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiyeno usiku Paulo anaona masomphenya.+ Munthu wina wa ku Makedoniya anaimirira ndi kumupempha kuti: “Wolokerani ku Makedoniya kuno mudzatithandize.” 2 Akorinto 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndipotu, pamene tinafika ku Makedoniya,+ thupi lathu silinapumule,+ koma masautso amitundumitundu anapitirizabe kutigwera.+ Kunja anali kulimbana nafe, mkati tinali kukhala mwamantha.
9 Ndiyeno usiku Paulo anaona masomphenya.+ Munthu wina wa ku Makedoniya anaimirira ndi kumupempha kuti: “Wolokerani ku Makedoniya kuno mudzatithandize.”
5 Ndipotu, pamene tinafika ku Makedoniya,+ thupi lathu silinapumule,+ koma masautso amitundumitundu anapitirizabe kutigwera.+ Kunja anali kulimbana nafe, mkati tinali kukhala mwamantha.